Onerani vidiyoyi kuti mulimbitse chikhulupiriro chanu komanso kuti mudziwe mmene kukhala munthu wauzimu kumatithandizira kuzindikira mmene ulosi unakwaniritsidwira.