Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

“Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye Ndi Khristu”

“Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye Ndi Khristu” (Mbali Yoyamba)

“Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye Ndi Khristu” (Mbali Yoyamba)

N’chiyani chimakupangitsani kukhulupirira kuti Mulungu anamuika Yesu kukhala Ambuye ndi Khristu? Onerani vidiyoyi kuti ikuthandizeni kukumbukira mfundo zosonyeza kuti Mulungu anaikadi Yesu kukhala Ambuye ndi Khristu.

Onaninso

Yesu Ndi Mesiya Amene Mulungu Ananeneratu Kuti Adzabwera

Yesu anakwaniritsa maulosi onse a m’Baibulo onena za Mesiya. Werengani m’Baibulo lanu kuti muone umboni wosonyeza kuti maulosi onse onena za Mesiya anakwaniritsidwadi.

Zimene Baibulo Limanena Zokhudza Mesiya

Kodi mukudziwa kuti Baibulo linalosera kuti Mesiya adzafa asanamalize ntchito yake?

Yesu—Ndi Njira, Choonadi Ndi Moyo

Werengani bukuli kuti mudziwe zonse zimene zinachitika pa moyo wa Yesu monga mmene Baibulo limafotokozera.