Yobu anakumana ndi mavuto otsatizana omwe anayesa kwambiri chikhulupiriro chake. Vidiyoyi ikufotokoza za banja la a Banda lomwe linakumananso ndi mavuto motsatizana. Kodi n’chiyani chinawathandiza kuti asataye mtima pa nthawi imeneyi?