Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

‘Palibe Ngakhale Mawu Amodzi Omwe Sanakwaniritsidwe’

Aisiraeli anali atayenda zaka zambiri m’chipululu ndipo n’kuti atatsala pang’ono kulowa m’Dziko Lolonjezedwa. Ndiye kodi Aisiraeli, omwe pa nthawiyo ankatsogoleredwa ndi Yoswa, akanapitirizabe kumvera Yehova n’kuona malonjezo ake akukwaniritsidwa? Onerani vidiyoyi yomwe ikusonyeza zimene zinawachitikira. Vidiyoyi ikuthandizani kuti musamakayikire zimene Mulungu walonjeza.