Koperani masewero a nkhani za m’Baibulo ndipo mungapeze phunziro lofunika kwambiri m’masewero amenewa. Mungaphunzirenso mfundo zina zofunika kwambiri zokhudza anthu otchulidwa m’Baibulo komanso zinthu zina zomwe zinachitika.

Sankhani chinenero chimene mukufuna pa kabokosi ka zinenero, kenako dinani kabatani ka Fufuzani kuti muone masewero omwe alipo m’chinenerocho. Lembani mawu amodzi kapena awiri a dzina la sewero limene mukufuna.