Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA November 2015 | Kodi Mulungu Amagwirizana Ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo?

Mungadabwe ndi zimene Baibulo limanena pa nkhaniyi.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mulungu Amagwirizana Ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo?

M’nthawi ya Aisiraeli, Mulungu ankalamula anthu ake kumenya nkhondo. Koma kenako, Yesu anauza otsatira ake kuti azikonda adani awo. Kodi Mulungu anali atasintha maganizo?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mulungu Ankagwirizana Ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo M’nthawi ya Aisiraeli?

Pali mfundo zitatu zokhudza nkhondo zimene Mulungu ankalamula anthu ake kumenya.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mulungu Ankagwirizana Ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo M’nthawi ya Atumwi?

Maganizo a Mulungu sanasinthe pa nkhani ya nkhondo, koma kodi n’chifukwa chiyani Mulungu sanathandize Ayuda ngati mmene ankachitira ndi Aisiraeli?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mulungu Amagwirizana Ndi Zoti Anthu Azimenya Nkhondo Masiku Ano?

Posachedwapa Mulungu adzabweretsa nkhondo imene idzathetse nkhondo zonse.

Kodi Mukudziwa?

N’chifukwa chiyani Yosefe anayamba wameta asanakaonane ndi Farao? N’chifukwa chiyani Baibulo limanena kuti bambo a Timoteyo anali Mgiriki?

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Ndinkaona Ngati Zinthu Zikundiyendera

A Pawel Pyzara anali munthu wa makhalidwe oipa komanso ankafuna ntchito yapamwamba. Koma tsiku lina anasintha atamenyedwa ndi anthu 8

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

“Mwana Wanga Wokondedwa Ndi Wokhulupirika Mwa Ambuye”

Kodi n’chiyani chinathandiza Timoteyo kukhala Mkhristu wolimba mtima ngakhale kuti poyamba anali wamanyazi?

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi anthu oukitsidwa adzakhala kuti?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Nkhondo ya Aramagedo Idzakhala Yotani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibulo, koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imatchulidwa m’Baibulo lonse.