Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA June 2015 | Kodi Sayansi Ingalowe M’malo mwa Baibulo?

Kodi mfundo za sayansi zimagwirizana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa kapena zimatsutsana?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Sayansi Imatithandiza Bwanji?

Ndi mfundo iti ya sayansi yomwe imawachititsa kutsutsa zoti kuli Mulungu?

NKHANI YAPACHIKUTO

Sayansi Singatithandize Kudziwa Zonse

Ponena mbiri ya sayansi, wasayansi wina dzina lake Carl Sagan analemba kuti: “Wasayansi, ngakhale wanzeru kwambiri akhoza kupeza zinthu zomwe si zolondola.”

Mungatani Kuti Muzisangalalabe Ngakhale Mutakalamba?

Werengani magaziniyi kuti mudziwe mfundo 6 zomwe zingakuthandizeni kuti muzisangalala ngakhale mutakalamba.

MBIRI YA MOYO WANGA

Chuma Chomwe Chakhala ku banja Lathu kwa Mibadwo 7

Kevin Williams akufotokoza zokhudza anthu a m’banja lake omwe akhala akutumikira Yehova.

Kodi Okana Khristu Ndi Ndani?

Kodi okana Khristu adzabwera m’tsogolo, kapena akhala alipo kuyambira kale?

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi mungatani kuti ana anu akule bwino?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Nkhani Zimene Zili M’Baibulo Ndi Nzeru za Anthu?

Taonani mfundo yochititsa chidwi iyi imene ili m’Baibulo.