Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA April 2015 | Kodi Mungakonde Kuphunzira Baibulo?

Anthu ambiri padziko lonse ali ndi mwayi wophunzira Baibulo ndi a Mboni za Yehova. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene kuphunzira Baibulo kungakuthandizireni.

NKHANI YAPACHIKUTO

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kuphunzira Baibulo?

Kodi mumaona kuti simungapeze nthawi yophunzira Baibulo komanso kuti kuphunzira Baibulo n’kovuta? Kapena mumaopa kupangana ndi wa Mboni kuti azikuphunzitsani Baibulo chifukwa choona kuti zimenezi n’zopanikiza?

Mwayi Woti Aliyense Aphunzire Baibulo

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mayankho a mafunso 8 omwe anthu amakonda kufunsa okhudza phunziro la Baibulo.

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Mafunso Atatu Omwe Anasintha Moyo Wanga

Mphunzitsi anaphunzitsidwa ndi mwana wake wasukulu. Doris Eldred anapeza mayankho ogwira mtima a mafunso ake.

Anapeza Zinthu Zamtengo Wapatali Pamulu wa Zinyalala

Kachidutswa komwe Roberts anapeza ka Uthenga Wabwino wa Yohane, ndiye kachidutswa kakale kwambiri ka Baibulo.

KUCHEZA NDI MUNTHU WINA

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukumbukira Imfa ya Yesu?

Anthu ambiri amakumbukira imfa ya Yesu pa Khristu pa Khirisimasi ndi kuuka kwake Isitala. N’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova amakumbukira imfa ya Yesu, osati kubadwa kwake?

Kodi Mukudziwa?

Kodi kapitawo wa asilikali achiroma ankagwira ntchito yotani? Kodi magalasi odziyang’anira akale anali osiyana bwanji ndi a masiku ano?

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi n’zotheka kuti anthu padziko lonse lapansi azidzakondana?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Baibulo Ndi Lochokera kwa Mulungu?

Anthu ambiri amene analemba Baibulo amati analemba maganizo a Mulungu. N’chifukwa chiyani amatero?