Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA August 2013 | Kodi Kuonera Zolaula Kuli Ndi Mavuto Otani?

Kodi kuonera zolaula kuli ndi mavuto otani? Kodi munthu angatani kuti asiye kuonera zolaula?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Kuonera Zolaula Kuli Ndi Mavuto Otani?

Kodi kuonera zolaula kumakhudza bwanji anthu komanso mabanja?

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

“Ndinayamba Kuganizira Kwambiri za Moyo Wanga”

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene Baibulo linathandizira munthu wina kusiya makhalidwe oipa komanso maganizo ake kuti ayambe kusangalatsa Mulungu.

ZIMENE OWERENGA AMAFUNSA

N’chifukwa Chiyani Anthu Ena Ofotokozedwa M’Baibulo Sanatchulidwe Mayina Awo?

Kodi tinganene kuti anthu amene anafotokozedwa m’Baibulo osatchulidwa mayina awo anali oipa kapena osafunika?

YANDIKIRANI MULUNGU

“Makhalidwe a Mulungu Osaoneka ndi Maso Akuonekera Bwino”

Kodi mumakhulupirira kuti kuli Mulungu? Kodi mungatchule umboni wosonyeza kuti iye alipo?

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Anapulumutsidwa “Pamodzi ndi Anthu Ena 7”

Kodi Nowa ndi banja lake anapulumuka bwanji chigumula chomwe chinachitika padziko lonse lapansi?

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

N’chifukwa chiyani Mulungu sasangalala ndi mapemphero ena? Nanga ifeyo tingatani kuti Mulungu azimvetsera mapemphero athu?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi a Mboni za Yehova Amapewa Anthu Amene Kale Anali M’chipembedzo Chawo?

Nthawi zina zimakhala zoyenerera kuti munthu achotsedwe mumpingo ndipo zimenezi zimathandiza kuti munthuyo asinthe n’kubwereranso mumpingo.