Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA January 2013 | Kodi Muyenera Kuopa Kutha kwa Dzikoli?

Malinga ndi zimene Baibulo limanena, kodi ”kutha kwa dziko” kumatanthauza chiyani?

Kwa Owerenga Magazini Athu

Kuyambira ndi magazini ino ya January 2013, pazisankhidwa nkhani kuchokera m’magazini ino zomwe zizipezeka pa intaneti pokha. Werengani kuti mudziwe chifukwa chake pakhala kusintha kumeneku.

NKHANI YAPACHIKUTO

Nkhani ya Kutha kwa Dziko, Kodi Ndi Yoopsa, Yosangalatsa Kapena Yokhumudwitsa?

Mungadabwe ndi zimene Baibulo limanena pa nkhani ya kutha kwa dziko.

YANDIKIRANI MULUNGU

“Mwaziulula kwa Tiana”

Werengani za zimene mungachite kuti mudziwe zoona zenizeni zokhudza Mulungu zomwe zimapezeka m’Baibulo.

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

“Ndinapeza Ufulu Weniweni”

Werengani kuti mudziwe mmene Baibulo lathandizira mnyamata wina kusiya kusuta fodya, mankhwala osokoneza bongo komanso kumwa mowa mwauchidakwa.

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

“Ngakhale Kuti Anafa, Iye Akulankhulabe”

Werengani kuti mudziwe zifukwa zitatu zimene zinachititsa kuti Abele azikhulupirira kwambiri Mlengi wathu wachikondi.

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi dzina la Mulungu ndani ndipo n’chifukwa chiyani tiyenera kumaligwiritsa ntchito?

Zina zimene zili pawebusaiti

Pewani Nsanje

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Mose anachita atayamba kunyozedwa ndi Aroni ndi Miriamu, omwe anali abale ake.

Uzinena Kuti, “Zikomo Kwambiri”

Makolo, muzithandiza ana anu, ngakhale aang’ono kwambiri, kuti adziwe kufunika konena kuti, “Zikomo kwambiri.”