NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) June 2015

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa July 27 mpaka pa August 30, 2015.

Khristu Ndiye Mphamvu ya Mulungu

Zozizwitsa za Yesu zinkathandiza anthu kalelo ku Isiraeli koma zimasonyezanso zimene adzachitire anthu posachedwapa.

He Loved People

Kodi zoziziwitsa za Yesu zimasonyeza kuti iye amaona bwanji anthu?

N’zotheka Kukhalabe Oyera

Baibulo limatchula zinthu zitatu zimene zingatithandize kuti tisamaganizire zoipa.

“Ngati Kingsley Akukwanitsa, Kuli Bwanji Ine?”

Kingsley wa ku Sri Lanka anali ndi mavuto aakulu koma anachita khama kwambiri kuti akwanitse kuwerenga Baibulo kwa maminitsi ochepa.

Tizichita Zinthu Mogwirizana ndi Pemphero la Ambuye—Gawo 1

N’chifukwa chiyani Yesu anayamba pemphero lake ndi mawu akuti “Atate wathu” osati “Atate wanga”?

Tizichita Zinthu Mogwirizana ndi Pemphero la Ambuye—Gawo 2

Pemphero lakuti mutipatse chakudya chathu chalero limatanthauza zambiri.

“Mukufunika Kupirira”

Yehova watipatsa zinthu 4 zimene zingatithandize kupirira mavuto.

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga mosamala magazini aposachedwapa a Nsanja ya Olonda? Tayesani kuyankha mafunso otsatirawa.