Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) November 2013

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira kuleza mtima kwa Mulungu pamene tikuyembekezera kuti Yehova awononge dziko loipali? Kodi masiku ano Yehova ndi Yesu amaweta bwanji nkhosa zawo za padziko lapansi?

“Khalani Maso Kuti Musanyalanyaze Kupemphera”

N’chifukwa chiyani Akhristu oona afunika kupemphera kosalekeza? Kodi kupempherera anthu ena kumathandiza ndani?

Kodi Tingathandize Bwanji Anthu Ena?

Werengani nkhaniyi kuti muone mmene gulu lathu limagwiritsira ntchito zopereka pothandiza anthu ena.

Pitirizani ‘Kuyembekezera Moleza Mtima’

Kodi ndi zinthu ziti zimene zidzasonyeza kuti mapeto a dziko loipali akufika? Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira kuleza mtima kwa Mulungu?

MBIRI YA MOYO WANGA

Kutumikira Mulungu Kuli Ngati Mankhwala Ake

Onesmus anabadwa ndi matenda a mafupa. Onani mmene malonjezo a m’Baibulo amulimbikitsira

Kodi Abusa 7 ndi Atsogoleri 8 Akuimira Ndani Masiku Ano?

Kodi Hezekiya, Yesaya, Mika ndi akalonga a ku Yerusalemu anasonyeza bwanji kuti anali abusa abwino? Nanga abusa 7 ndi atsogoleri 8 akuimira ndani masiku ano?

Muzimvera Abusa Amene Yehova Watipatsa

Akulu anaikidwa ndi mzimu woyera kuti aziweta nkhosa mumpingo wa Mulungu. N’chifukwa chiyani nkhosa ziyenera kuwamvera?

Abusa, Tsanzirani Abusa Aakulu

Kodi akulu angathandize bwanji Mkhristu amene akudwala mwauzimu? Kodi akulu angatsanzire bwanji Yehova ndi Yesu Khristu omwe ndi abusa aakulu?

KALE LATHU

“Ndinali Ngati Kamba Woyenda Ndi Chigoba Chake”

Chakumapeto kwa chaka cha 1929, kunali mavuto aakulu a zachuma. Kodi akopotala kapena kuti apainiya ankapeza bwanji zinthu zofunika pamoyo wawo?