Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) August 2013

Magaziniyi ikufotokoza zimene tingachite kuti tikhalebe oyera, tikhale oyenera kugwira ntchito ya Mulungu, tipewe kuimba Mulungu mlandu pa mavuto athu komanso kuti tisafooke kapena kukhumudwa.

Mwapatulidwa

Onani zinthu 4 zimene zingatithandize kukhalabe oyera ndiponso kuti Mulungu azitigwiritsa ntchito.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi n’zoyenera kuti makolo achikhristu azikhala pamodzi ndi mwana wawo wochotsedwa pa misonkhano yampingo?

MBIRI YA MOYO WANGA

Yehova ‘Amanyamula Katundu Wanga Tsiku ndi Tsiku’

Kodi n’chiyani chathandiza mlongo wina wa ku Namibia kuchita upainiya kwa zaka zoposa 20 ngakhale kuti amadwaladwala?

‘Musakwiyire Yehova’

Anthu ena amakwiyira Mulungu mumtima mwawo. Amamuimba mlandu pa mavuto awo. Kodi tingapewe bwanji msampha umenewu?

Makolo, Phunzitsani Ana Anu Kuyambira Ali Akhanda

Kodi makolo ayenera kuyamba liti kuphunzitsa mwana wawo? Kodi ayenera kumuphunzitsa bwanji?

Tiziganizirana Ndiponso Kulimbikitsana

Kodi tingalimbikitsane bwanji kuti tipitirize kutumikira Mulungu mokhulupirika ngakhale pamene tikukumana ndi mavuto?

Ganizirani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala

Satana safuna kuti Mulungu azisangalala nafe. Kodi tingateteze bwanji ubwenzi wathu ndi Yehova?

Elisa Anaona Magaleta Oyaka Moto, Kodi Inunso Mukuwaona?

Elisa ankakhulupirira kwambiri Yehova ndiponso kumudalira ndi mtima wonse. Kodi tikuphunzira chiyani pa chitsanzo chake?

KALE LATHU

Mfumu Inasangalala Kwambiri

Werengani kuti mumve mmene mfumu ya ku Swaziland inkakondera kuphunzira Baibulo.