Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) February 2013

Magaziniyi ikufotokoza cholowa chapadera chimene tili nacho monga anthu a Yehova. Ikufotokozanso zimene tingachite kuti tikhale m’chitetezo cha Yehova.

Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu

Kuganizira zimene Yehova wachitira mtundu wa anthu komanso atumiki ake kungakuthandizeni kuyamikira kwambiri cholowa chochokera kwa Mulungu.

Kodi Timayamikira Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu?

Kudziwa kuti muli ndi cholowa chochokera kwa Mulungu kungakuthandizeni kuti mukhalebe okhulupirika kwa Mulungu.

Paulo Analalikira Msilikali Woteteza Mfumu

Paulo ankalalikira nthawi iliyonse. Werengani kuti mudziwe zimene tingachite potengera chitsanzo cha Paulo.

Khalanibe Otetezeka M’chigwa cha Yehova

Kodi chigwa chachitetezo ndi chiyani, ndipo anthu amene amalambira Yehova angatetezedwe bwanji m’chigwa chimenechi?

Samalani ndi Zolinga za Mtima Wanu

Nthawi zina mtima wathu ungaikire kumbuyo zoipa zimene tachita. Kodi n’chiyani chingatithandize kudziwa zimene zili mumtima mwathu?

Musalole Chilichonse Kukulepheretsani Kupeza Ulemerero

Kodi mungapeze bwanji ulemerero wochokera kwa Mulungu? Kodi n’chiyani chingakulepheretseni kupeza ulemererowo?

Anali Wochokera M’banja la Kayafa

Kupezeka kwa bokosi la mafupa a Miriamu ndi umboni woti Baibulo limafotokoza za anthu enieni komanso mabanja awo.

KALE LATHU

Sewero la Chilengedwe Linali la pa Nthawi Yake

Werengani kuti mudziwe mmene ”Sewero la Chilengedwe” linathandizira a Mboni za Yehova ku Germany pa nthawi imene ankazunzidwa pa nkhondo yachiwiri yapadziko lonse.