Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) July 2016

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira August 29 mpaka September 25, 2016.

Anadzipereka ndi Mtima Wonse—Ku Ghana

Anthu amene anasamukira m’mayiko ena amakumana ndi mavuto ambiri koma amadalitsidwanso kwabasi.

Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina

Yesu anafotokoza chifukwa chake sitiyenera kumangotanganidwa ndi kufunafuna chuma.

N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kukhalabe Maso’?

Pali zinthu zitatu zimene titapanda kusamala zingatilepheretse kukhala maso.

“Usachite Mantha. Ineyo Ndikuthandiza”

Yehova wakhala akuthandiza anthu pa nthawi ya mavuto.

Tiziyamikira Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu

Kodi njira yaikulu imene Mulungu anasonyezera anthu kukoma mtima kwakukulu ndi iti?

Tizilalikira Uthenga wa Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu

Kodi ntchito yolalikira ‘uthenga wabwino wa Ufumu’ imasonyeza bwanji kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi zimene Ezekieli anauzidwa kuti aphatikize ndodo ziwiri n’kukhala imodzi zikuimira chiyani?