Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

BAIBULO

 • Kuphunzira Kuzikusangalatsani Komanso Kuzikuthandizani, July

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

 • Anthu Opereka zabwino amene Yesu anawatchula anali ndani? Nov.

 • Kodi Paulo “anakwatulidwira kumwamba kwachitatu” komanso ‘kulowa m’paradaiso’?​—2 Akor. 12:2-4, Dec.

 • N’chifukwa chiyani mawu a pa Salimo 144:12-15 anasinthidwa? Apr.

 • Ngati mwamuna ndi mkazi amene sali pa banja atakhala limodzi usiku, pangafunike komiti yoweruza? July

 • Paulo anali wadazi? Mar.

 • Tiziika pa webusaiti kapena pa intaneti zimene gulu lafalitsa? Apr.

MBIRI YA MOYO WANGA

 • Ndakhala Ndikulimbikitsidwa pa Mavuto Anga Onse (E. Bazely), June

 • Ndayesetsa Kuti Ndisagwe Ulesi (M. Danyleyko), Aug.

 • Ndinali Wosauka Koma Panopa Ndine Wolemera (S. Herd), May

 • Yehova Sanandigwiritsepo Mwala! (E. Bright), Mar.

 • Yehova Wandidalitsa Kwambiri Chifukwa cha Zimene Ndinasankha (C. Molohan), Oct.

 • ‘Yehova Watichitira Zinthu Zabwino’ (J. Bockaert), Dec.

 • Zinthu Zonse N’zotheka ndi Yehova (B. Berdibaev), Feb.

MBONI ZA YEHOVA

 • Akhristu Achikulire, Yehova Amayamikira Kukhulupirika Kwanu, Sept.

 • Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Madagascar, Jan.

 • Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Myanmar, July

 • Anayamba Kufesa Mbewu za Ufumu ku Portugal Aug.

 • Kodi Akulu ndi Atumiki Othandiza Angaphunzire Chiyani kwa Timoteyo? Apr.

 • Kodi Ndingapereke Chiyani kwa Yehova? (zopereka), Nov.

 • Nkhani za Onse Zinathandiza Kufalitsa Uthenga Wabwino (Ireland), Feb.

 • Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo mu 1918, Oct.

 • Zokolola N’zochuluka (Ukraine), May

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

 • Chimwemwe Ndi Khalidwe Limene Mulungu Amapereka, Feb.

 • Kukoma Mtima Ndi Khalidwe Limene Limasonyezedwa M’mawu ndi Zochita, Nov.

 • Kuleza Mtima Ndi Kupirira Kokhala ndi Cholinga, Aug.

 • Kupatsana Moni N’kothandiza Kwambiri, June

 • Mtendere, Kodi Mungaupeze Bwanji? May

 • Muzichitira Chifundo Anthu, July

 • “Wolungama adzakondwera mwa Yehova,” Dec.

NKHANI ZOPHUNZIRA

 • Achinyamata, Kodi Mukuyesetsa Kukwaniritsa Zolinga Zauzimu? Apr.

 • Achinyamata, Mlengi Wanu Amafuna Kuti Muzikhala Osangalala, Dec.

 • Achinyamata, Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wosangalala, Dec.

 • Achinyamata, Musasunthike Polimbana ndi Mdyerekezi, May

 • Anthu Amene Amatumikira “Mulungu Wachimwemwe” Amakhala Osangalala, Sept.

 • Anthu Opatsa Amakhala Osangalala, Aug.

 • Chikumbutso Chimatithandiza Kukhala Ogwirizana, Jan.

 • “Gula Choonadi Ndipo Usachigulitse,” Nov.

 • “Iye Amapereka Mphamvu kwa Munthu Wotopa,” Jan.

 • Kodi Kukhala Munthu Wauzimu Kumatanthauza Chiyani? Feb.

 • Kodi Maso Anu Amayang’ana kwa Ndani? July

 • Kodi Mukudziwa Nkhani Yonse? Aug.

 • Kodi Mumadziwa Yehova Ngati Mmene Nowa, Danieli ndi Yobu Ankamudziwira? Feb.

 • Kodi Mumafuna Kukhala Wodziwika kwa Ndani? July

 • Kodi Mumamudziwa Bwino Mdani Wanu? May

 • Kodi Mumayendera Maganizo a Ndani? Nov.

 • Kodi Tingapeze Bwanji Ufulu Weniweni? Apr.

 • Kodi Tiyenera Kukonda Ndani Kuti Tikhale Osangalala? Jan.

 • Kuchereza Alendo Ndi Kofunika Kwambiri, Mar.

 • Makolo, Kodi Mukuthandiza Ana Anu Kuti Ayenerere Kubatizidwa? Mar.

 • Mulungu Amatilangiza Chifukwa Chotikonda, Mar.

 • Munthu Ayenera Kubatizidwa Kuti Akhale Mkhristu, Mar.

 • Muzikhulupirira Yehova Kuti Mukhale ndi Moyo, Nov.

 • Muziphunzitsa Chikumbumtima Chanu ndi Malamulo Komanso Mfundo za Mulungu, June

 • “Mverani Malangizo Kuti Mukhale Anzeru,” Mar.

 • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupereka kwa Amene Ali ndi Chilichonse? Jan.

 • N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kupitiriza Kubala Zipatso Zambiri’? May

 • “Ndani Ali Kumbali ya Yehova?” July

 • “Ndidzayenda M’choonadi Chanu,” Nov.

 • Ndife Anthu a Yehova, July

 • “Ngati Zimenezi Mukuzidziwa, Ndinu Odala Mukamazichita,” Sept.

 • “Onetsani Kuwala Kwanu” Kuti Yehova Alemekezeke, June

 • Pitirizani Kukula Mwauzimu, Feb.

 • Pitirizani Kusonyeza Chikondi Chifukwa Chimalimbikitsa, Sept.

 • “Tidzaonana M’Paradaiso,” Dec.

 • Tisamaweruze Poona Maonekedwe Akunja, Aug.

 • Tizigwira Ntchito ndi Yehova Tsiku Lililonse, Aug.

 • Tizikhala Okhulupirika Komanso Omvera Ngati Nowa, Danieli ndi Yobu, Feb.

 • Tizikhala Okoma Mtima Komanso Oganizira Ena Ngati Yehova, Sept.

 • Tizikhala Osiyana ndi Anthu a M’dzikoli, Jan.

 • Tizikhalabe ndi Mtendere Wamumtima Zinthu Zikasintha, Oct.

 • Tizikhulupirira Khristu Yemwe Ndi Mtsogoleri Wathu, Oct.

 • Tizilankhula Zoona Zokhazokha, Oct.

 • Tizilemekeza “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi,” Dec.

 • Tizilimbikitsana Ndipo “Tiwonjezere Kuchita Zimenezi,” Apr.

 • Tiziphunzitsa Mfundo za Choonadi, Oct.

 • Tizitsanzira Yehova pa Nkhani Yolimbikitsa Ena, Apr.

 • Tizitumikira Yehova Mulungu Amene Amapereka Ufulu, Apr.

 • Tiziyendera Maganizo a Yehova? Nov.

 • Tonsefe Tikhale Ogwirizana Ngati Yehova ndi Yesu, June

 • “Ufumu Wanga Suli Mbali ya Dziko Lino,” June

 • Yehova Amakonda Anthu Amene ‘Amabereka Zipatso’ Mopirira, May

 • Yehova Ndi Wamphamvuyonse Koma Amaganizira Ena, Sept.

NKHANI ZOSIYANASIYANA

 • Akanatha Kusangalatsa Mulungu (Rehobowamu), June

 • Chilamulo cha Mose pothetsa nkhani za tsiku ndi tsiku, Jan.

 • Nthawi Ili Bwanji? (nthawi yotchulidwa m’Baibulo), Sept.

 • Sitefano anakhalabe wodekha pamene ankazunzidwa?, Oct.

NSANJA YA OLONDA YOGAWIRA

 • Kodi Baibulo Ndi Lothandizabe Masiku Ano? Na. 1

 • Kodi M’tsogolomu Muli Zotani? Na. 2

 • Kodi Mulungu Zimam’khudza Mukamavutika? Na. 3

GALAMUKANI!

 • Mfundo Zothandiza Amene Aferedwa, Na. 3

 • Mfundo Zothandiza Kuti Banja Liziyenda Bwino, Na. 2

 • Mungatani Kuti Muzikhala Wosangalala? Na. 1