Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) August 2018

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa October 1-28, 2018.

Kodi Mukudziwa Nkhani Yonse?

Kodi ndi mfundo zitatu ziti za m’Baibulo zimene zingatithandize kuganizira bwino nkhani iliyonse n’kuzindikira zoona zake?

Tisamaweruze Poona Maonekedwe Akunja

Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zitatu zimene tiyenera kupewa pa nkhani yoweruza anthu.

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndayesetsa Kuti Ndisagwe Ulesi

Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zosangalatsa zimene Maxim Danyleyko wakumana nazo pa zaka 68 zimene wakhala akuchita umishonale.

Anthu Opatsa Amakhala Osangalala

Kodi kukhala opatsa kumathandiza bwanji kuti munthu akhale wosangalala?

Tizigwira Ntchito ndi Yehova Tsiku Lililonse

Kodi tingagwire ntchito ndi Yehova m’njira 5 ziti?

Kuleza Mtima Ndi Kupirira Kokhala ndi Cholinga

Nkhaniyi ikusonyeza tanthauzo la kuleza mtima, zimene tingachite kuti tikhale ndi khalidweli komanso ubwino wake.

KALE LATHU

Anayamba Kufesa Mbewu za Ufumu ku Portugal

Kodi anthu anakumana ndi mavuto ati pamene anayamba kulalikira ku Portugal, nanga anathana nawo bwanji?