Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) August 2016

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira September 26 mpaka October 23, 2016.

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndakhala Moyo Wosangalala Chifukwa Chothandiza Ena

Mnyamata wa ku England anayamba kukhala moyo wosangalala ndipo kenako anakhala mmishonale ku Puerto Rico.

Kodi Ukwati Unayamba Bwanji Nanga Cholinga Chake N’chiyani?

Kodi n’zoona kuti ukwati ndi mphatso yochokera kwa Mulungu?

Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino?

Werengani nkhaniyi kuti mupeze malangizo othandiza.

Muzifufuza Chuma Chamtengo Wapatali Kuposa Golide

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene munthu amene amachita khama kuphunzira Baibulo amafananira ndi ofufuza golide.

Kodi Tingatani Kuti Tizichita Zambiri M’gulu la Yehova?

Werengani nkhaniyi kuti mupeze yankho la funsoli.

Kodi Kuphunzitsa Ena N’kofunika Bwanji?

Kodi mungawathandize kukhala ndi zolinga ziti?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

N’chifukwa chiyani anthu amene ankatsutsa Yesu ankaona kuti kusamba m’manja ndi nkhani yaikulu?

KALE LATHU

“Ndikugwira Ntchito Yotamanda Yehova”

Ophunzira Baibulo sankadziwa zambiri pa nkhani yosalowerera ndale koma ankachitabe zinthu moona mtima ndipo zotsatira zake zinali zabwino.