Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) May 2017

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa July 3 mpaka 30, 2017.

Tizithandiza Alendo Kuti ‘Azitumikira Yehova Mokondwera’

Kodi tingalalikire bwanji anthu othawa kwawo amene sadziwa Yehova?

Kodi Tingathandize Bwanji Ana a Anthu Ochokera M’mayiko Ena?

Ngati ndinu kholo limene lasamukira m’dziko lina, kodi mungathandize bwanji ana anu kuti adziwe Yehova? Nanga anthu ena angakuthandizeni bwanji?

MBIRI YA MOYO WANGA

Vuto Losamva Silinandilepheretse Kuphunzitsa Anthu Ena Baibulo

Walter Markin ali ndi vuto losamva koma wakhala ndi moyo wosangalatsa kwambiri potumikira Yehova Mulungu.

Musalole Kuti Chikondi Chanu Chizirale

Akhristu ena akale anasiya chikondi chimene anali nacho poyamba. N’chiyani chingatithandize kuti tizikondabe kwambiri Yehova?

“Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”

Yesu anaphunzitsa Simoni Petulo zimene ayenera kuika pamalo oyamba. Kodi masiku ano tingatsatirenso zimene Yesu anaphunzitsazo?

Kodi Gayo Ankathandiza Bwanji Akhristu Anzake?

Kodi Gayo anali ndani, nanga n’chifukwa chiyani tiyenera kumutsanzira?

Moyo Wosalira Zambiri Ndi Wosangalatsa

N’chiyani chinathandiza banja lina kuti liyambe moyo wosalira zambiri? Kodi banjali linachita zotani? N’chifukwa chiyani tinganene kuti zomwe anachita zinawathandiza kukhala osangalala?

KALE LATHU

“Tinalimbikitsidwa Kukonda Kwambiri Yehova Ndiponso Kulalikira Mwakhama”

Msonkhano wachigawo wa mu 1922 utachitika, kodi anthu anatsatira bwanji malangizo oti ‘alengeze za Mfumu ndi Ufumu wake’?