Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) January 2016

Nsanjayi ili ndi nkhani zophunzira kuyambira February 29 mpaka April 3, 2016.

Anadzipereka Ndi Mtima Wonse ku Oceania

Kodi a Mboni za Yehova amene anasamukira komwe kulibe ofalitsa ambiri ku Oceania amatani akakumana mavuto?

“Mupitirize Kukonda Abale”

Lemba la chaka cha 2016 lingatithandize kukonzekera mavuto amene tikumane nawo posachedwapa.

Tiziyamikira ‘Mphatso Yaulere’ Imene Mulungu Anatipatsa

Kodi chikondi cha Mulungu chimatithandiza bwanji kuti tizitsatira Yesu mosamala kwambiri, tizikonda abale athu komanso kuti tizikhululukira ena?

Mzimu Umachitira Umboni Limodzi ndi Mzimu Wathu

Kodi n’chiyani chimachitika munthu akadzozedwa? Nanga amadzozedwa bwanji?

“Tipita Nanu Limodzi”

Kodi tiyenera kukumbukira chiyani zokhudza a 144,000?

Timasangalala Kwambiri Kugwira Ntchito Limodzi ndi Mulungu

Kodi kugwira ntchito ndi Mulungu kumathandiza bwanji kuti tizisangalala komanso kuti tikhale otetezeka?