Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) February 2016

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira April 4 mpaka May 1, 2016.

MBIRI YA MOYO WANGA

Yehova Wandithandiza Kwambiri Pomutumikira

A Corwin Robison anatumikira Mulungu mokhulupirika kwa zaka 73, ndipo zaka zoposa 60 pa zaka zimenezi, anatumikira pa Beteli ya ku United States.

Abulahamu Anali “Bwenzi” la Yehova

Kodi mukufuna kukhala bwenzi la Yehova? Chitsanzo cha Abulahamu chingakuthandizeni.

Tsanzirani Anthu Amene Anali pa Ubwenzi Wolimba ndi Yehova

Kodi n’chiyani chinathandiza Rute, Hezekiya komanso Mariya kuti akhale pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu?

Kodi Mungatani Kuti Muzitumikirabe Yehova Mosangalala?

Mfundo zitatu zimene mukamaziganizira zingakuthandizeni kuti muzitumikirabe Yehova mosangalala.

Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova

Chitsanzo cha Yonatani chingatithandize kukhala okhulupirika kwa Yehova pa mavuto osiyanasiyana.

Tizitsanzira Atumiki a Yehova Amene Anali Okhulupirika

Kodi Davide, Yonatani, Natani ndiponso Husai anasonyeza bwanji kuti anali okhulupirika kwa Yehova kuposa kwa wina aliyense?

KALE LATHU

Galimoto Yodziwika Kwambiri Yokhala ndi Zokuzira Mawu

Kuchokera mu 1936 mpaka 1941, galimoto ya zokuzira mawu inathandiza a Mboni za Yehova ochepa a ku Brazil kuti athe kulalikira uthenga wa Ufumu kwa anthu ambiri m’dzikoli.