Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2016

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2016

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

 • Lefèvre d’Étaples (womasulira mabuku), Na. 6

 • Machaputala ndi Mavesi, Na. 2

 • Mmene Linapulumukira, Na. 4

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

 • Ndikhaleko Mosangalala Komanso Mwamtendere kwa Chaka Chimodzi (A. Broggio), Na. 1

 • Ndinali Waukali Komanso Sindinkachedwa Kuyambitsa Ndewu (A. De la Fuente), Na. 5

 • Ndinasintha Movutikira Kwambiri (J. Mutke), Na. 4

 • Ndinayamba Kulemekeza Akazi (J. Ehrenbogen), Na. 3

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

 • Kodi anthu a Mulungu analowa liti mu ukapolo wa m’Babulo Wamkulu? Mar.

 • Kodi odzozedwa amalandira bwanji “chikole” nanga amadindidwa bwanji “chidindo”? (2 Akor 1:21, 22), Apr.

 • Kodi Satana anapitadi ndi Yesu kukachisi? (Mat. 4:5; Luka 4:9), Mar.

 • Kupereka ndalama kwa ogwira ntchito m’boma, May

 • Kuphatikiza ndodo ziwiri (Ezek. 37), July

 • Kusangalala munthu akabwezeretsedwa, May

 • Kuwinduka kwa madzi apadziwe la Betesida (Yoh. 5:7), May

 • “Mawu a Mulungu” pa Aheberi 4:12, Sept.

 • Munthu wa kachikwama konyamulira inki ndi amuna 6 okhala ndi zida (Ezek. 9:2), June

 • Nkhani ya kusamba m’manja (Maliko 7:5), Aug.

MBIRI YA MOYO

 • Kukhala “Zinthu Zonse kwa Anthu Osiyanasiyana” (D. Hopkinson), Dec.

 • Masisitere Anasintha N’kukhala Alongo (F. ndi A. Fernández), Apr.

 • Ndilibe Manja Koma Ndinalandira Choonadi (B. Merten), Na. 6

 • Ndimasangalala Chifukwa Chothandiza Ena (R. Parkin), Aug.

 • Ndimayesetsa Kutengera Anthu a Zitsanzo Zabwino (T. McLain), Oct.

 • Yehova Wandithandiza Kwambiri Pomutumikira (C. Robison), Feb.

MBONI ZA YEHOVA

 • Anadzipereka ndi Mtima Wonse, ku Ghana, July

 • Anadzipereka ndi Mtima Wonse, ku Oceania, Jan.

 • Galimoto Yodziwika Yokhala ndi Zokuzira Mawu (Brazil), Feb.

 • “Kwa Amene Apatsidwa Ntchitoyi” (msonkhano wachigawo wa ku Cedar Point, Ohio, U.S.A.), May

 • Muzilola Kuti Yehova Azikutsogolerani (zomwe zinachitikira a Mboni ena), Sept.

 • “Ndikugwira Ntchito Yotamanda Yehova” (Germany, nkhondo yoyamba ya padziko lonse), Aug.

 • “Ntchitoyi Ndi Yaikulu” (zopereka), Nov.

 • “Ofalitsa a ku Britain Galamukani!” (1937), Nov.

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

 • Anateteza Uthenga Wabwino kwa Akuluakulu a Boma, Sept.

 • Chuma Chamtengo Wapatali Kuposa Golide (nzeru zochokera kwa Mulungu), Aug.

 • Khalidwe la Mtengo Wapatali Kuposa Dayamondi (kuona mtima), June

 • Kodi Utumiki Wanu Uli Ngati Mame? Apr.

 • Kupemphera mu Akachisi? Na. 2

 • Luso Loona Zinthu M’maganizo Mwathu, Apr.

 • ‘Mumasunga Nzeru Zopindulitsa’? Oct.

 • Mungatani Kuti Muzitumikirabe Yehova Mosangalala, Feb.

 • Mungathandize Bwanji Mpingo Wanu? Mar.

 • Munthu Wofatsa Amasonyeza Nzeru, Dec.

 • Musamade Nkhawa, Na. 1

 • Musamakhale Mwamantha, Na. 1

 • Muzitsanzira Aneneri, Mar.

 • Kuchita Zinthu Moona Mtima? Na. 1

NKHANI ZOPHUNZIRA

 • Abulahamu Anali “Bwenzi” la Yehova,” Feb.

 • Achinyamata, Kodi Mungakonzekere Bwanji Kubatizidwa? Mar.

 • Achinyamata, Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa? Mar.

 • Achinyamata, Yesetsani Kulimbitsa Chikhulupiriro Chanu, Sept.

 • Anatuluka mu Babulo Wamkulu, Nov.

 • Anthu a Mulungu Anaitanidwa Kuchoka Mumdima, Nov.

 • Kodi Baibulo Likusinthabe Moyo Wanu? May

 • Kodi Kuphunzitsa Ena N’kofunika Bwanji? Aug.

 • Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu? Sept.

 • Kodi Mumalola Kuti Yehova Azikuumbani? June

 • Kodi Mumaona Kuti Baibulo Ndi Buku Lapadera? Nov.

 • Kodi Mumasankha Bwanji Zochita? May

 • Kodi Mumathetsa Nkhani Mwachikondi Mukasemphana Maganizo? May

 • Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino? Aug.

 • Kodi Tingatani Kuti Tizichita Zambiri M’gulu la Yehova? Aug.

 • Kodi Tingathandize Bwanji Kulimbitsa Mgwirizano Wathu? Mar.

 • Kodi Ukwati Unayamba Bwanji Nanga Cholinga Chake N’chiyani? Aug.

 • Kodi Zinthu Zonse Zimene Yehova Amatipatsa Zimakuthandizani? May

 • ‘Kuika Maganizo pa Zinthu za Mzimu Kumabweretsa Moyo ndi Mtendere,’ Dec.

 • Manja Anu ‘Asalefuke,’ Sept.

 • Mawu a Mulungu Amatithandiza Kuti Tizichita Zinthu Mwadongosolo, Nov.

 • “Mulole Kuti Kupirira Kumalize Kugwira Ntchito Yake,” Apr.

 • Mungatani Kuti Mukhalebe Olimba Mwauzimu Mumpingo wa Chilankhulo China? Oct.

 • “Mupitirize Kukonda Abale,” Jan.

 • “Musaiwale Kuchereza Alendo,” Oct.

 • Musakhale Mbali ya Dzikoli, Apr.

 • Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina, July

 • Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova, Feb.

 • Muzikhulupirira Kwambiri Zinthu Zimene Mukuyembekezera, Oct.

 • Muzimutulira Yehova Nkhawa Zanu Zonse, Dec.

 • Muzisonyeza Kuti Mumakhulupirira Malonjezo a Yehova, Oct.

 • Muzithandiza Ana Anu Kuti Akhale ndi Chikhulupiriro Cholimba, , Sept.

 • Mzimu Umachitira Umboni Limodzi ndi Mzimu Wathu, Jan.

 • N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kukhalabe Maso’? July

 • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonkhana? Apr.

 • “Pitani Mukaphunzitse Anthu a Mitundu Yonse,” May

 • Pitirizani Kulimbana ndi Zimene Zingakulepheretseni Kupeza Madalitso, Sept.

 • Timasangalala Kwambiri Kugwira Ntchito Limodzi ndi Mulungu, Jan.

 • Tinamasulidwa ku Uchimo Chifukwa cha Kukoma Mtima Kwakukulu, Dec.

 • “Tipita Nanu Limodzi,” Jan.

 • Tipitirize Kulimbikitsana Tsiku ndi Tsiku, Nov.

 • Tisasiye Kutumikira Yehova Chifukwa cha Zochita za Ena, June

 • Tizilalikira Uthenga wa Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu, July

 • Tiziyamikira ‘Mphatso Yaulere’ Imene Mulungu Anatipatsa, Jan.

 • Tiziyamikira Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu, July

 • Tiziyamikira Kuti Yehova Amatiumba, June

 • Tsanzirani Anthu Amene Anali pa Ubwenzi Wolimba ndi Yehova, Feb.

 • Tsanzirani Atumiki a Yehova Amene Anali Okhulupirika, Feb.

 • Yehova Amadalitsa Anthu Okhulupirika, Apr.

 • Yehova Amapereka Mphoto kwa Anthu Omufunafuna ndi Mtima Wonse, Dec.

 • Yehova Amatsogolera Anthu Ake Kuti Adzapeze Moyo, Mar.

 • “Yehova Mulungu Wathu ndi Yehova Mmodzi,” June

NKHANI ZOSIYANASIYANA

 • Ansembe Aakulu M’Malemba Achigiriki, Na. 1

 • Aroma Ankapereka Ufulu kwa Ayuda a ku Yudeya, Oct.

 • Atsogoleri Achipembedzo Chachiyuda Ankalola Munthu Kuthetsa Ukwati pa Zifukwa Ziti? Na. 4

 • “Inde Ndipita” (Rabeka), Na. 3

 • Kodi Anthu Anayambitsa Kupembedza? Na. 4

 • Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira? Na. 1

 • Kodi Mdyerekezi ndi Ndani? Na. 2

 • Kodi Mungayerekezere Zomwe Mumakhulupirira Ndi Zimene Baibulo Limaphunzitsa? Na. 4

 • Kodi Munthu Ankafesadi Namsongole M’munda wa Mnzake? Oct.

 • Kodi Munthu Ayenera Kukhala M’chipembedzo Chinachake? Na. 4

 • Kodi Ndani Angatithandize Tikakhala pa Mavuto? Na. 5

 • Kodi Nkhani ya Davide ndi Goliyati Inachitikadi? Na. 5

 • Kodi Tiyenera Kukhala Mwanjira Inayake Popemphera? Na. 6

 • Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? Na. 5

 • Kodi Zachiwawa Zidzatha Padzikoli? Na. 4

 • Kumvera Chenjezo, Na. 2

 • Masomphenya Osonyeza Amene Ali Kumwamba, Na. 6

 • Mawu Olimbikitsa Kwambiri! (“mwana wanga”), Nov.

 • Mipukutu Yakale, Na. 1

 • Mulungu Amayankha Mapemphero Onse? Na. 6

 • Munthu Yemwe Munkamukonda Akamwalira, Na. 3

 • Utoto Komanso Nsalu Zimene Anthu Akale Ankagwiritsa Ntchito, Na. 3

 • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo” (Davide), Na. 5

 • Zimene Tingaphunzire kwa Mbalame, Na. 6

YEHOVA

 • “Amakuderani Nkhawa,” June

 • Dzina la Mulungu, Na. 3

 • “Usachite Mantha. Ineyo Ndikuthandiza” July

YESU KHRISTU

 • Ankasiyana Ndi Arabi Pochita Zinthu Ndi Akhate, Na. 4

 • Bambo a Yosefe, Na. 3

 • N’chifukwa Chiyani Anavutika Mpaka Kufa? Na. 2