Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

NSANJA YA OLONDA Na. 6 2017 | Kodi Mphatso Yamtengo Wapatali Kwambiri Ndi Iti?

KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?

Kodi ndi ndani amene anatipatsa mphatso yabwino kwambiri kuposa zonse?

Baibulo limati: “Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba, pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo.”​Yakobo 1:17.

Nsanja ya Olonda iyi ikutithandiza kudziwa mphatso imene Mulungu watipatsa yomwe ndi yaikulu kuposa mphatso zonse.

 

NKHANI YAPACHIKUTO

“Ndinali Ndisanapatsidwepo Mphatso Yamtengo Wapatali Ngati Imeneyi”

Kodi mumafuna kupereka kapena kupatsidwa mphatso yabwino kwambiri?

NKHANI YAPACHIKUTO

Zimene Mungachite Kuti Mphatso Ikhale Yabwino Kwambiri

Sizophweka kupeza mphatso imene ingakhale yabwino kwambiri kwa munthu. Ndipotu kuti mphatso ikhale yabwino, zimadalira mmene munthu wopatsidwayo akuionera

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mphatso Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse Ndi Iti?

Pa mphatso zonse zimene Mulungu anatipatsa, pali imodzi yomwe ndi yamtengo wapatali kuposa zonse.

Kodi Yesu Ankaoneka Bwanji?

Kwa zaka zambiri anthu aluso akhala akujambula zithunzi zosiyanasiyana zoyerekezera mmene Yesu ankaonekera. Koma kodi Malemba amasonyeza kuti Yesu ankaoneka bwanji?

Kodi Tizitani Tikalakwitsa Zinthu?

Tonse timalakwitsa zinthu ndipo zilibe kanthu kuti tili ndi zaka zingati. Kodi tizitani tikalakwitsa?

N’chifukwa Chiyani Pali Mabaibulo Osiyanasiyana?

Mfundo yomwe ingakuthandizeni kudziwe chifukwa chake pali Mabaibulo osiyanasiyana.

Kodi Akhristu Ayenera Kukondwerera Khirisimasi?

Kodi atumwi a Yesu komanso ophunzira ake ankakondwerera Khirisimasi?

Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Mawu akuti Aramagedo amachititsa mantha anthu ambiri, koma kodi mawuwa amanena za chiyani?

Zina zimene zili pawebusaiti

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Khirisimasi?

Anthu ambiri amakondwererabe Khirisimasi ngakhale kuti amadziwa chiyambi chake. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake a Mboni za Yehova sakondwerera Khirisimasi.