Kodi tingapeze kuti mfundo zomwe zingatithandize tikaferedwa?

Nkhani za m’magaziniyi zikufotokoza zimene zimachitika munthu amene timamukonda akamwalira. Zikufotokozanso zimene mungachite kuti muthe kupirira mukaferedwa.