Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Galamukani!  |  Na. 2 2017

Kodi Mungakonde Kumvetsa Zimene Baibulo Limaphunzitsa?

Kodi Mungakonde Kumvetsa Zimene Baibulo Limaphunzitsa?

Simufunika

  • Kukhala wophunzira kwambiri

  • Kukhala ndi ndalama

  • Kumangokhulupirira zilizonse

Mukufunika

  • Kukhala ndi “luntha la kuganiza.”Aroma 12:1

  • Kukhala wodzichepetsa

Zimene Baibulo limaphunzitsa zingakudabwitseni.