Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

GALAMUKANI! October 2015 | Mafunso Atatu Omwe Anthu Amafuna Atafunsa Mulungu

Anthu ambiri amaona kuti zipembedzo zikulephera kuyankha mafunso ofunika kwambiri okhudza moyo. Komabe Baibulo lili ndi mayankho a mafunso amene anthu amakonda kufunsa.

NKHANI YAPACHIKUTO

Mafunso Atatu Omwe Anthu Amafuna Atafunsa Mulungu

N’chifukwa chiyani munatilenga? N’chifukwa chiyani mumalola kuti tizivutika? N’chifukwa chiyani anthu ambiri opemphera amachita zachinyengo?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Gulo Wakhungu Lodabwitsa Kwambiri

Kodi zimatheka bwanji kuti guloyu azimwa madzi pongogunditsa mchira kapena miyendo yake m’madzi?

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kodi Zamoyo Zinachita Kusintha?

Kodi zimene Baibulo limanena zoti zinthu zinachita kulengedwa, zimatsutsana ndi zimene asayansi amanena?

ANTHU NDI MAYIKO

Dziko la Uzbekistan

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri za dziko la Uzbekistan komanso chifukwa chake afabeti yawo yakhala ikusintha.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Kodi Mukufuna Kubwereranso Kunyumba?

Kodi zinthu zakuvutani ndipo mukuona kuti mukufunikanso kubwerera kwanu? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mfundo zomwe zingakuthandizeni kuti zinthu ziyambenso kukuyenderani bwino.

Kodi Mungathandize Bwanji Mnzanu Kapena Wachibale Akadwala?

Anthu ambiri amada nkhawa akauzidwa kuti agonekedwa m’chipatala kapena azipita kukaonana ndi dokotala. Kodi mungathandize bwanji mnzanu kapena wachibale akadwala?

ZOCHITIKA PADZIKOLI

Nkhani Zokhudza Mabanja

Kodi mabanja masiku ano akukumana ndi mavuto otani? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe kumene mungapeze malangizo amene angakuthandizeni kuti mukhale ndi banja labwino.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 1: N’chifukwa Chiyani Ndimakhulupirira Kuti Kuli Mulungu?

Kodi mungakonde kuti muzifotokozera ena molimba mtima zimene mumakhulupirira zoti kuli Mulungu? Werengani nkhaniyi kuti mupeze mfundo zimene zingakuthandizeni kuyankha ngati munthu wina wakufunsani zimene mumakhulupirira.

Phunziro 9: “Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse”

Kodi ukudziwa zinthu zimene Mulungu anayambirira kulenga? Onera vidiyoyi kuti udziwe mmene Mulungu analengera zinthu zosiyanasiyana.