Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

GALAMUKANI! APRIL 2015

N’chifukwa Chiyani Ana a Masiku Ano Safuna Kuuzidwa Zochita?

Makolo omwe amafuna kuphunzitsa ana awo makhalidwe abwino akumakumana ndi mavuto ambiri. Kodi chachititsa n’chiyani kuti zinthu zifike pamenepa?

N’chifukwa Chiyani Ana a Masiku Ano Safuna Kuuzidwa Zochita?

Kodi zomwe akatswiri ankanena zaka za m’ma 1960 zikukhudzabe mmene makolo ambiri amalerera ana awo masiku ano?

Kodi Malangizo Abwino Olerera Ana Mungawapeze Kuti?

Mfundo 5 za m’Baibulo zothandiza makolo kulera bwino ana awo.

Dziko la Honduras

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zokhudza anthu a ku Honduras.

Kodi Mungatani Ngati Mumasowa Wocheza Naye?

Kusowa ocheza nawo kwa nthawi yaitali kumasokoneza thanzi la munthu mofanana ndi mmene zimakhalira ndi munthu yemwe amasuta ndudu 15 pa tsiku. Kodi mungatani ngati nthawi zina mumaona kuti mumangokhala nokhanokha ndipo mukusowa wocheza naye?

Nyama

Kodi tiyenera kuziona bwanji nyama?

Musamagwiritse Ntchito Zipangizo Zamakono Monyanyira

Dzifunseni mafunso 4 kuti muone ngati mukugwiritsa ntchito zipangizo zamakono monyanyira.

Tindevu ta Mphaka

N’chifukwa chiyani asayansi akupanga maloboti okhala ndi zinthu zogwira ntchito ngati tindevu ta mphaka?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Kusewera Magemu a Pazipangizo Zamakono?

Mwina simunaganizirepo ubwino komanso kuipa kosewera magemu.

Uzikhululuka ndi Mtima Wonse

Kodi munthu akakuchitirani choipa muyenera kumutani?