Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

GALAMUKANI! JANUARY 2015

Kodi Moyo Unayamba Bwanji?

Kodi yankho la funsoli lingatengere ngati mumakhulupirira kuti kuli Mulungu kapena ayi?

Kodi Moyo Unayamba Bwanji?

N’chifukwa chiyani asayansi ena zimawavuta kukhulupirira kuti zamoyo zinasintha kuchokera ku zinthu zina?

Mafunso Awiri Omwe Tiyenera Kudziwa Mayankho Ake

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe ngati muyenera kukhulupirira zimene anthu omwe amati zamoyo zinasintha kuchokera ku zinthu zina amanena.

Baibulo Lili Ndi Mayankho Ogwira Mtima

Kodi n’chiyani chinathandiza wasayansi yemwe ankalimbikitsa anthu kuti asamakhulupirire Mulungu, kuti ayambe kukhulupirira Mulungu?

Chisa cha Njuchi

Kodi njuchi zakhala zikudziwa zinthu zotani zokhudza kugwiritsa ntchito malo mosamala zomwe akatswiri a masamu azitulukira posachedwapa mu 1999?

Mungatani Kuti Muziugwira Mtima?

Mfundo 5 zokuthandizani kuti muziugwira mtima.

Dziko la Costa Rica

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake anthu a m’dzikoli amadziwika kuti Atiko.

“Ndimayesetsa Kuti Ndisamangoganizira za Matenda Anga”

N’chiyani chimathandiza Elisa kupirira komanso kuiwalako matenda ake?

Mavuto

Kodi Mulungu amamva bwanji tikamavutika?

Nkhani Zokhudza Zipembedzo

Nkhani zaposachedwapa zikusonyeza kuti zipembedzo zalephera kugwirizanitsa anthu.

Zina zimene zili pawebusaiti

N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuonerera Zolaula?

Kodi kuonera zolaula n’kofanana motani ndi kusuta fodya?

Uzikhala Wokoma Mtima Ndiponso Wopatsa

Onerani kuti mudziwe mmene Kalebe ndi Sofiya amasangalalira akamagawana zinthu.