Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo

Kalozera wa Mafanizo

Kalozera wa Mafanizo

Manambalawa akusonyeza mutu umene fanizolo likupezeka

mbalame komanso maluwa 35

kumanga nsanja 84

ngamila ikhoza kulowa pa diso la singano 96

ana amene anakhala pansi mumsika 39

kusankha malo olemekezeka 83

alimi anapha mwana wa mwiniwake wa munda 106

aganyu anawapatsa ndalama ya dinari 97

ndalama ya dalakima inapezeka 85

khoka 43

kapolo wokhulupirira ndi wanzeru 111

woyang’anira nyumba wokhulupirika 78

bambo amafunitsitsa kupatsa ana ake zinthu zabwino 35

mtengo wa mkuyu 79

M’busa Wabwino 80

asodzi a anthu 22

maziko a nyumba 35

kambewu ka tirigu kamafa, kenako kamamera 103

nkhuku ya thadzi imasonkhanitsa ana ake 110

nyumba yomangidwa pathanthwe 35

kuitanira anthu osauka ku phwando 83

mfumu inakhululuka ngongole yaikulu 64

mfumu imene ikufuna kukamenya nkhondo 84

mfumu inakonza phwando la ukwati 107

ufa wosakaniza ndi zofufumitsa 43

zofufumitsa za Afarisi 58

ndalama ya dalakima imene inasowa 85

nkhosa yosochera 63

anthu anakana ataitanidwa 83

ndalama ya mina 100

alimi omwe anapha anthu 106

kambewu kampiru, chikhulupiriro 89

kambewu kampiru, Ufumu 43

chipata chopapatiza 35

diso la singano 96

Msamariya wachifundo 73

vinyo watsopano, matumba akale a vinyo 28

ngale ya mtengo wapatali 43

musamaponyere nkhumba ngale zanu 35

bwenzi lokakamira 74

mwana wotayika 86

wogwira pulawo 65

munthu wolemera komanso Lazaro 88

munthu wolemera yemwe anamanga nkhokwe zazikulu 77

mchere wa dziko 35

mbewu zinagwera panthaka yosiyanasiyana 43

kusokerera chigamba chatsopano pa nsalu yakale 28

nkhosa komanso mbuzi 114

kapolo amene akuchokera kumunda 89

akapolo amene ankayembekezera kubwera kwa mbuye wawo 78

mwana wotayika 86

wofesa mbewu 43

wofesa mbewu amene anagona 43

kusefa nyerere, kumeza ngamila 109

kachitsotso m’diso la m’bale wako 35

matalente 113

wokhometsa msonkho komanso Mfarisi 94

anamwali 10 112

chuma chomwe chinabisidwa m’munda 43

mtengo wa mpesa weniweni 120

ana awiri anatumidwa kuti apite kumunda wa mpesa 106

anthu awiri amene anabwereka ndalama 40

mizimu yonyansa inabwerera 42

kapolo wosakhululuka 64

woyang’anira nyumba wosalungama 87

tirigu ndi namsongole 43

mkazi wamasiye ndi woweruza 94

ogwira ntchito m’munda wa mpesa 97

KALOZERA WA MABOKOSI

‘Masiku Akuti Ayeretsedwe Anakwanira’ 6

Maulendo Osangalatsa 10

Kodi Asamariya Anachokera Kuti? 19

Munthu Wogwidwa Ndi Mzimu Woipa 23

Mafanizo Onena za Kusala Kudya 28

Ankabwereza Mfundo Pophunzitsa 35

Thukuta la Yesu Linaoneka Ngati Madontho a Magazi 123

Munda wa Magazi 127

Kukwapula 129

“M’pachikeni” 132