Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo

 Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa

Bukuli likufotokoza za moyo komanso utumiki umene Yesu anachita. Likufotokozanso kuti anali munthu wotani, zimene anaphunzitsa, zimene anachita komanso zimene ifeyo tingaphunzirepo.

Bukuli sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.

Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.

Malemba onse m’bukuli achokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

Losindikizidwa mu February 2015

Chichewa (jy-CN)