Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Yandikirani kwa Yehova

 CHIGAWO CHACHITATU

“Wa Mtima Wanzeru”

“Wa Mtima Wanzeru”

Nzeru yeniyeni ndi mtundu umodzi wa chuma chamtengo wapatali chimene munthu angachifunefune. Yehova yekha ndiye gwero la nzeru zoterozo. M’chigawo chino, tifufuza mozama nzeru zopanda malire za Yehova Mulungu, amene munthu wokhulupirika Yobu anamunena kuti: “Ndiye wa mtima wanzeru.”—Yobu 9:4.

M'CHIGAWO ICHI

MUTU 17

‘Ha! Kuya Kwake kwa Nzeru za Mulungu!’

N’chifukwa chiyani nzeru za Mulungu zimaposa, kudziwa kwake zinthu, kumvetsa komanso kuzindikira?

MUTU 18

Nzeru mu “Mawu a Mulungu”

N’chifukwa chiyani Mulungu anagwiritsa ntchito anthu kulemba Baibulo mmalo mogwiritsa ntchito angelo kapena kulemba yekha?

GAWO 19

“Nzeru ya Mulungu M’chinsinsi Chopatulika”

Kodi pangano latsopano lomwe kale Mulungu analibisa ndipo tsopano analiulula ndi lotani?

MUTU 20

“Wa Mtima Wanzeru”—Komatu Wodzichepetsa

Kodi n’zotheka bwanji kuti Mlengi wachilengedwe chonse akhale wodzipetsa?

MUTU 21

Yesu Anaulula “Nzeru ya kwa Mulungu”

Kodi Yesu ankaphunzitsa bwanji kuti asilikali omwe anatumidwa kukamugwira abwereko chimanjamanja?

MUTU 22

Kodi ‘nzeru ya Kumwamba’ Ikugwira Ntchito mwa Inu?

Baibulo limafotokoza njira 4 zimene zingakuthandizeni kupeza nzeru ya Mulungu kapena kuti nzeru ‘yochokera kumwamba.’