Mulungu amafuna kuti anthu amitundu yonse azilankhula naye kudzera m’pemphero. Koma kodi Mulungu amamvetsera kapena kuvomereza mapemphero onse?