Baibulo limanena kuti malemba onse ndi ochokera kwa Mulungu ndipo iye “sanganame.” (1 Atesalonika 2:13; Tito 1:2) Kodi zimenezi ndi zoona kapena Baibulo ndi buku la nthano chabe?