Yesu anafotokoza kwambiri za Ufumu wa Mulungu kuposa nkhani ina iliyonse. Koma kodi Ufumu umenewu ndi chiyani? Nanga kodi udzatichitira chiyani?