• Kodi Imfa Inatengapo Munthu Amene Munakonda?

  • Kodi mudakali ndi chisoni?

  • Kodi mukufunikira chithandizo pachisoni chanucho?

  • Kodi pali chiyembekezo cha akufa?

  • Ngati zili tero, kodi icho nchotani?

  • Kodi tingatsimikizire motani?

M’brosha lino, mafunso oterowo adzapatsidwa mayankho otonthoza ochokera m’Baibulo. Tikupemphani kuliŵerenga mosamalitsa.