Kabukuka sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.

Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.

Malemba onse m’kabuku kano achokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza lina. Komabe, Chichewa chake tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures​—With References.

Kosindikizidwa mu August 2017

Chichewa (we-CN)