Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha

Mlengi akufuna kutitsogolera, kutiteteza komanso kutidalitsa.

Mawu Oyamba

Mulungu amakonda anthu ndipo amawaphunzitsa kuti zinthu ziziwayendera bwino.

Kodi Mulungu Amalankhula Nafe Motani?

Tiyenera kudziwa zoyenera kuchita komanso amene angatithandize kuzichita.

Kodi Mulungu Woona Ndani?

Tingadziwe dzina lake komanso makhalidwe ake.

Kodi Moyo Unali Wotani m’Paradaiso?

Buku loyamba la m’Baibulo limafotokoza za moyo wa m’Paradaiso.

Kodi Yesu Anali Ndani?

N’chifukwa chiyani tiyenera kudziwa bwino Yesu?

Kodi Imfa ya Yesu Imakukhudzani bwanji?

Imathandiza kuti tidzapeze madalitso osaneneka.

Kodi Paradaiso Adzabwera Liti?

Baibulo linaneneratu zimene zidzachitike Paradaiso akayandikira.

Kodi Anthu Omvera Mulungu Adzalandira Madalitso Otani?

Zinthu zimene mukulakalaka kudzaona.

Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu?

Kodi ndi zinthu ziti zimene mungatchule m’mapemphero anu?

Kodi Mungatani Kuti Aliyense M’banja Mwanu Azisangalala?

Mulungu amene anayambitsa banja amapereka malangizo abwino kwambiri.

Kodi Tiyenera Kuchita Chiyani Kuti Tikondweretse Mulungu?

Pali zinthu zina zimene Mulungu amadana nazo komanso zimene amakondwera nazo.

Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova?

Zimene mumasankha kuchita ndi zomwe zimasonyeza ngati muli wokhulupirika.