Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2017-2018​—Womwe Padzakhale Woyang’anira Dera

Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. N’chifukwa chiyani timavutika kuchita zabwino? (1 Pet. 5:8; Aroma 12:2; 7:21-25)

  2. Kodi munthu amene akufesa zopindulitsa thupi amachita chiyani, nanga tingapewe bwanji kufesa zopindulitsa thupi? (Agal. 6:8)

  3. Kodi ndi ndani amene tiyenera ‘kuwachitira zabwino’? (Agal. 6:10)

  4. Kodi tingatani kuti tizifesa motsatira mzimu wa Mulungu? (Agal. 6:8)

  5. Kodi tidzakolola chiyani tikapanda kutopa? (Agal. 6:9)