M’MAWA

 • 9:30 Kumvetsera Nyimbo

 • 9:40 Nyimbo Na. 77 ndi Pemphero

 • 9:50 N’chifukwa Chiyani Timavutika Kuchita Zabwino?

 • 10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzipewa Kufesa Zopindulitsa Thupi

  • Muzigwiritsa Ntchito Malo Ochezera a pa Intaneti Moyenera

  • Muzisankha Zosangalatsa Zabwino

  • Muzipewa Mtima Wansanje

  • Konzani Tsogolo Labwino

 • 11:05 Nyimbo Na. 45 ndi Zilengezo

 • 11:15 Pitirizani Kuchitira Onse Zabwino

 • 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

 • 12:00 Nyimbo Na. 63

 MASANA

 • 1:10 Kumvetsera Nyimbo

 • 1:20 Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero

 • 1:30 Nkhani ya Onse:Kodi Mungapewe Bwanji Kupusitsa Mulungu?

 • 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

 • 2:30 Nyimbo Na. 59 ndi Zilengezo

 • 2:40 Nkhani Yosiyirana: Pitirizani Kufesa Motsatira Mzimu wa Mulungu

  • Khalani ndi Chizolowezi Chophunzira

  • Muzigwiritsa Ntchito Mfundo za M’Baibulo Posankha Zochita

  • ‘Dzanja Lanu Lisapume’

 • 3:40 Tidzakolola Zabwino Tikapanda Kutopa

 • 4:15 Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero