Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2017-2018​​—Womwe Padzakhale Woimira Nthambi

Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. Kodi “chilamulo cha Khristu” n’chiyani? (Agal. 6:2)

  2. Kodi tingakwaniritse bwanji chilamulo cha Khristu ngakhale pamene anthu ena sakutiona? (1 Akor. 10:31)

  3. Kodi timakwaniritsa bwanji chilamulo cha Khristu tikamalalikira? (Luka 16:10; Mat. 22:39; Mac. 20:35)

  4. N’chifukwa chiyani tinganene kuti chilamulo cha Khristu ndi chabwino kwambiri kuposa Chilamulo cha Mose? (1 Pet. 2:16)

  5.   Kodi anthu apabanja komanso makolo angatani kuti azikwaniritsa chilamulo cha Khristu m’banja mwawo? (Aef. 5:22, 23, 25; Aheb. 5:13, 14)

  6. Kodi mungatani kuti muzikwaniritsa chilamulo cha Khristu mukakhala kusukulu? (Sal. 1:1-3; Yoh. 17:14)

  7. Kodi tingatani kuti tizikondana ngati mmene Yesu anatikondera? (Agal. 6:1-5, 10)