SALIMO 138:3

 M’MAWA

 • 9:30 Kumvetsera Nyimbo

 • 9:40 Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero

 • 9:50 Yehova Amatithandiza Kukhala Olimba Mtima

 • 10:05 Nkhani Yosiyirana: Khalani Olimba Mtima Ngati . . .

  • Inoki

  • Mose

  • Yehosafati

  • Petulo

 • 11:05 Nyimbo Na. 69 ndi Zilengezo

 • 11:15 Muzilimba Mtima mu Utumiki

 • 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

 • 12:00 Nyimbo Na. 48

 MASANA

 • 1:10 Kumvetsera Nyimbo

 • 1:20 Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero

 • 1:30 Nkhani ya Onse: Muzisonyeza Kuti Muli Kumbali ya Kulambira Koona

 • 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

 • 2:30 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo

 • 2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzilimba Mtima Ngati Yesu Mukamakumana ndi Mavuto

  • M’banja

  • Kusukulu

  • Kuntchito

  • Kumene Mumakhala

 • 3:40 Anthu Olimba Mtima Adzalandira “Mphoto Yaikulu Kwambiri”

 • 4:15 Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero