1. Kodi ndi ndani amene angatipatse mphamvu? (Yos. 1:9; Sal. 68:35)

  2. Kodi tingatani kuti tipitirize kulimbitsa chikhulupiriro chathu? (Aheb. 11:6)

  3. Kodi tikudziwa bwanji kuti tikhoza kugwira bwino ntchito imene Yehova watipatsa? (Hag. 2:4-9)

  4. Kodi Yehova amatithandiza bwanji tikakumana ndi mavuto aakulu? (Sal. 18:6, 30; Akol. 4:10, 11)

  5. N’chiyani chingathandize achinyamata komanso anthu amene ali pa banja kuti azikhala kumbali ya Yehova? (Mat. 22:37, 39)

  6. Kodi tingatani kuti ‘tikhale olimba m’chikhulupiriro komanso amphamvu’? (1 Akor. 16:13; Aroma 15:5; Aheb. 5:11–6:1; 12:16, 17)