Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mizimu ya Akufa Ilipodi?

Kodi Baibulo limaphunzitsa chiyani pa nkhani ya mmene akufa alili? Kodi anthu amene anamwalira angatithandize kapena kutichitira zoipa zinazake?

Mawu Oyamba

Anthu ambiri amakhulupirira kuti munthu akafa amapita kudziko lamizimu ndipo amatha kuona zimene anthu akuchita padziko lapansi pano. Kodi zimenezi ndi zoona?

Kodi Anthu Akafa Amapita Kudziko la Mizimu?

Mawu amene Mulungu anauza Adamu, yemwe anali munthu woyamba, amatithandiza kudziwa zimene zimachitika munthu akamwalira.

Yehova Analenga Angelo Ambirimbiri

M’masomphenya amene Mulungu anamuonetsa, Danieli anaona angelo okwana 100 miliyoni

Angelo Ena Anaukira Mulungu

Angelo ena anaukira Mulungu ndipo izi zinabweretsa mavuto kwa anthu.

Ziwanda Zimapha

Zitsanzo za m’Baibulo komanso za masiku ano zimasonyeza kuti Satana ndi ziwanda zake ndi oopsa ndipo amachitira anthu zinthu zoipa.

Ziwanda Zimanama Kuti Akufa Ali Moyo

Ziwanda zakwanitsa kusocheretsa anthu ambiri, koma Baibulo limathandiza anthu kudziwa kuti ziwanda ndi zabodza.

Ziwanda Zimafuna Kuti Tisamamvere Mulungu

Kuti zimenezi zitheke, zimasocheretsa anthu.

Muzitumikira Yehova Osati Satana

Mungadziwe bwanji kuti mwasankha zoyenera?

Moyo Udzakhala Wosangalatsa

Satana ndi ziwanda zake adzapatsidwa mpata woti asocheretse anthu kwa kanthawi. Kenako Yehova adzabweretsa madalitso kwa anthu onse.

Dzikoli Lidzakhala Paradaiso

Kodi zinthu zidzakhala bwanji Yehova akadzathetsa mavuto onse amene Satana anayambitsa m’dzikoli?