Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2017 la Mboni za Yehova Padziko Lonse

Onani zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yolalikira kuyambira mu September 2016 mpaka August 2017.

Ziwerengero Zonse za 2017

Lipotili likusonyeza zinthu zimene a Mboni za Yehova achita pogwira ntchito yawo yolalikira padziko lonse komanso zinthu zimene agwiritsa ntchito.

Lipoti la 2017 la Mayiko Komanso Madera

Lipotili likuphatikizapo chiwerengero cha Mboni za Yehova, obatizidwa, opezeka pa Chikumbutso komanso zinthu zina.