Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?

Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?

Kodi mayankhowo tingawapeze . . .

  • kwa asayansi?

  • kwa anthu anzeru?

  • m’Baibulo?

 WOLEMBA BAIBULO WINA ANAPEMPHA MULUNGU KUTI,

“Ndithandizeni kukhala wozindikira . . . Mawu anu onse ndi choonadi.”Salimo 119:144, 160, Baibulo la Dziko Latsopano.

Baibulo likuyankha mafunso a anthu ambiri.

Kodi mungakonde kukhala ena mwa anthu amenewo?

Webusaiti ya jw.org ingakuthandizeni kuyankha mafunso anu.

 PA MAFUNSO OFUNIKA KWAMBIRI OMWE ALI M’MUNSIWA KODI NDI FUNSO LITI LOMWE MUMAFUNA MUTADZIWA YANKHO LAKE?

Pezani mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso amenewa pa webusaiti ya jw.org.

(Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)

Onaninso

KODI NDANI AKUCHITA CHIFUNIRO CHA YEHOVA MASIKU ANO?

Kodi Pamalo Athu a pa Intaneti Pali Zinthu Zotani?

Mungadziwe zinthu zambiri zokhudza ifeyo komanso zimene timakhulupirira ndipo mungapeze mayankho okhudza Baibulo.