Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Bwererani kwa Yehova

Yehova amafufuza nkhosa zimene zasochera ndipo akukuitanani kuti mubwerere.

Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira

M’kalatayi Bungwe Lolamulira likupempha atumiki a Mulungu amene asochera kuti abwerere m’gulu lake.

GAWO 1

“Nkhosa Zosochera Ndidzazifunafuna”

Kodi Mulungu amaona kuti nkhosa yosochera ndi yokanika?

GAWO 2

Nkhawa—“Timapanikizidwa Mwamtundu Uliwonse”

Mwina pano mukuona kuti simukuchita zimene munkakwanitsa kale. M’nkhaniyi mupeza mfundo yokuthandizani kupeza mphamvu yochokera kwa Mulungu.

GAWO 3

Kukhumudwa—Tikakhala ndi “Chifukwa Chodandaulira”

Kuganizira mfundo zitatu za m’Baibulo kungakuthandizeni ngati Mkhristu wina anakukhumudwitsani.

GAWO 4

Kudziimba Mlandu—“Ndiyeretseni ku Tchimo Langa”

Kodi mungatani kuti musiye kudziimba mlandu?

GAWO 5

Bwererani kwa ‘M’busa Wanu ndi Woyang’anira Moyo Wanu’

Ngati ndikufuna kubwerera kwa Yehova ndingayambire pati? Kodi abale ndi alongo adzandilandira bwanji?

Mawu Omaliza

Kodi mumaganizira zinthu zosangalatsa zimene munkachita ndi anthu a Yehova?