Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017

Switzerland

Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse

Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse

 PADZIKO LONSE

  • MAYIKO 240

  • OFALITSA 8,340,847

  • NTHAWI IMENE TINATHERA POGWIRA NTCHITO YOLALIKIRA 1,983,763,754

  • MAPHUNZIRO A BAIBULO 10,115,264

M'CHIGAWO ICHI

Africa

Werengani zimene a Mboni ena anakumana nazo komanso zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yophunzitsa Baibulo ku Ghana, Guinea-Bissau, Liberia, Malawi, Togo komanso Sierra Leone.

America

Zimene a Mboni ena anakumana nazo ku Brazil, Haiti, Mexico, United States ndi Venezuela.

Asia ndi Middle East

Zimene zinachitika ku Hong Kong, Mongolia, Philippines ndi Sri Lanka.

Europe

Werengani zimene zinachitikira a Mboni ena a ku Azerbaijan, Britain, Bulgaria, Georgia, Denmark, Hungary, Norway ndi Ukraine.

Oceania

Nkhani zochititsa chidwi zochokera ku Australia, Guam, New Caledonia, Papua New Guinea ndi Timor-Leste.