Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 ZIMENE ZACHITIKA M’CHAKA CHAPITACHI

Zinthu Zikuyenda ku Warwick

Zinthu Zikuyenda ku Warwick

KU Warwick komwe kukumangidwa likulu lathu latsopano kuli ntchito yaikulu zedi. Abale ndi alongo ambiri akuchita zonse zimene angathe kuti agwire nawo ntchitoyi. Ndipo ambiri akumanena kuti: “Tikuona kuti ndi mwayi wamtengo wapatali kugwira nawo ntchitoyi.” Tamvani mmene ntchitoyi ikuyendera.