Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ziwerengero Zonse za 2015

Ziwerengero Zonse za 2015
 • Nthambi za Mboni za Yehova: 89

 • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 240

 • Mipingo Yonse: 118,016

 • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 19,862,783

 • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 15,177

 • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira: 8,220,105

 • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 7,987,279

 • Maperesenti a Mmene Ofalitsa Anawonjezekera Poyerekeza ndi 2014: 1.5

 • Obatizidwa Onse: 260,273

 • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 443,504

 • Avereji ya Apainiya Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,135,210

 • Maola Onse Amene Tinathera mu Utumiki: 1,933,473,727

 • Avereji ya Maphunziro a Baibulo Mwezi Uliwonse: 9,708,968

M’chaka cha utumiki cha 2015, Mboni za Yehova zinagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 236 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira dera pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 26,011 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.