Nkhani ya m’Baibulo ya pa Ekisodo chaputala 3 mpaka 5 imasonyeza kuti Mulungu amene anagawanitsa Nyanja Yofiira adzakupulumutsaninso inuyo ngati mutakhala ndi chikhulupiriro komanso mutapitirizabe kupirira.

Yochokera pa Ekisodo 3:​1-22; 4:​1-9; 5:​1-9; 6:​1-8; 7:​1-7; 14:​5-10, 13-31; 15:​1-21.